Kuvomeleza aliyense

Pamtima wa Ubuntu palichikhulupiliro chokuti Komputa ndiya aliyense. Podzela mpata wakutha kusankha chiyankhulo, mtundu komanso kakulidwe kamalemba, Ubuntu imapangitsa ntchito za komputa kuphweka - Aliyense kuli konse komwe muli.